Psalms 69:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwa abale anga ndasanduka mlendo, kwa ana a mai wanga ndili ngati wakudza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Abale anga andiyesa mlendo, ndi ana a mai wanga andiyesa wa mtundu wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndine mlendo kwa abale anga, munthu wakudza kwa ana aamuna a amayi anga;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Abale anga andiyesa mlendo, Ndi ana a mai wanga andiyesa wa mtundu wina.