Psalms 69:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Changu chochitira Nyumba yanu chandiphetsa, chipongwe cha anthu okunyozani chandigwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti changu cha pa nyumba yanu chandidya; ndi zotonza za iwo otonza Inu zandigwera ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti changu chochitira nyumba yanu chandiphetsa ndipo chipongwe cha iwo amene amanyoza Inu chandigwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cangu ca pa nyumba yanu candidya; Ndi zotonza za iwo otonza Inu zandigwera ine.