Psalms 7:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu ndiye muweruzi wolungama, amalanga anthu oipa nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu ndiye Woweruza wolungama, ndiye Mulungu wakukwiya masiku onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu amaweruza molungama, Mulungu amene amaonetsa ukali wake tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu ndiye Woweruza walungama, Ndiye Mulungu wakukwiya masiku onse.