Psalms 7:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wakonza zida zake zoopsa, waika mivi yamoto ku uta wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamkonzera zida za imfa; mivi yake aipanga ikhale yansakali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wakonza zida zake zoopsa; Iye wakonzekera mivi yake yoyaka moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamkonzera zida za imfa; Mibvi yace aipanga ikhale yansakali,