Psalms 7:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakumba mbuna kuti ikhale yozama, koma amagwamo ndiye yemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anachita dzenje, nalikumba, nagwa m'mbuna yomwe anaikumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amene akumba dzenje ndi kulizamitsa amagwera mʼdzenje limene wakumbalo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anacita dzenje, nalikumba, Nagwa m'mbuna yomwe anaikumba.