Psalms 7:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choipa chitsata mwini, chiwawa chimabwerera pa mwini wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chovuta chake chidzambwerera mwini, ndi chiwawa chake chidzamgwera pakati pamutu pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mavuto amene amayambitsa amamubwerera mwini; chiwawa chake chimatsikira pa mutu wake womwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cobvuta cace cidzambwerera mwini, Ndi ciwawa cace cidzamgwera pakati pamutu pace.