Psalms 7:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidzathokoza Chauta chifukwa cha kulungama kwake, ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina la Chauta, Wopambanazonse uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzayamika Yehova monga mwa chilungamo chake; ndipo ndidzaimbira Yehova Wam'mwambamwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzayamika Yehova chifukwa cha chilungamo chake; ndipo ndidzayimba nyimbo zamatamando pa dzina la Yehova Wammwambamwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzayamika Yehova monga mwa cilungamo cace; Ndipo ndidzayimbira Yehova Wam'mwambamwamba.