Psalms 7:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti iwo anganding'ambe ngati mkango, ndi kundikadzula popanda wina wondipulumutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti angamwetule moyo wanga ngati mkango, ndi kuukadzula, wopanda wina wondilanditsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mwina angandikadzule ngati mkango, ndi kundingʼamba popanda wondipulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti angamwetule moyo wanga ngati mkango, Ndi kuukadzula, wopanda wina wondilanditsa.