Psalms 7:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta Mulungu wanga, ngati ndachita izi: kumchimwira munthu aliyense,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita ichi; ngati m'manja anga muli chosalungama;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova Mulungu wanga, ngati ndachita izi ndipo ndapezeka wolakwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova Mulungu wanga, ngati ndacita ici; Ngati m'manja anga muli cosalungama;