Psalms 7:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kubwezera choipa bwenzi langa, kapena kumulanda zinthu mdani wanga popanda chifukwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati ndambwezera choipa iye woyanjana ndine; (inde, ndamlanditsa wondisautsa kopanda chifukwa);
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati ndachita zoyipa kwa iye amene ndili naye pa mtendere, kapena popanda chifukwa ndalanda mdani wanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndambwezera coipa iye woyanjana ndine; (Inde, ndamlanditsa wondisautsa kopanda cifukwa);