Psalms 7:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mdaniyo andithamangitse ndi kundigwira, andipondereze pansi ndi kundipha, andisiye ndili thasa m'fumbi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mdani alondole moyo wanga, naupeze; naupondereze pansi moyo wanga, naukhalitse ulemu wanga m'fumbi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamenepo lolani adani anga andithamangitse ndi kundipitirira, lolani kuti moyo wanga aupondereze pansi ndipo mundigoneke pa fumbi. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mdani alondole moyo wanga, naupeze; Naupondereze pansi moyo wanga, Naukhalitse ulemu wanga m'pfumbi.