Psalms 7:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyamukani, Inu Chauta, muli okwiya, mulimbane ndi adani anga aukali. Dzambatukani, Inu Mulungu wanga, amene mwalamula kuti chilungamo chichitike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukani Yehova mu mkwiyo wanu, nyamukani chifukwa cha ukali wa akundisautsa; ndipo mugalamukire ine; mwalamulira chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyamukani Yehova, mu mkwiyo wanu; nyamukani kutsutsana ndi mkwiyo wa adani anga. Dzukani Mulungu wanga, lamulirani chilungamo chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukani Yehova mu mkwiyo wanu, Nyamukani cifukwa ca ukali wa akundisautsa: Ndipo mugalamukire ine; mwalamulira ciweruzo.