Psalms 7:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amagamula milandu ya anthu. Tsono thetsani mlandu, Inu Chauta, moyenera, popeza kuti ine sindidalakwe konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova aweruza anthu mlandu; mundiweruze, Yehova, monga mwa chilungamo changa, ndi ungwiro wanga uli mwa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova aweruzeni anthu a mitundu inayo. Ndiweruzeni Yehova, monga mwa chilungamo changa, monga mwa moyo wanga wangwiro, Inu Wammwambamwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova aweruza anthu mlandu: Mundiweruze, Yehova, monga mwa cilungamo canga, ndi ungwiro wanga uli mwa ine.