Psalms 7:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thetsani ntchito zoipa za anthu ochimwa, koma anthu ochita zabwino muŵabwezere zokoma. Inu ndinu amene mumayesa maganizo ndi mitima yomwe, Inu ndinu Mulungu wolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ithe mphulupulu ya anthu oipa, ndikupemphani, koma wolungamayo mumkhazikitse. Pakuti woyesa mitima ndi impso ndiye Mulungu wolungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Mulungu wolungama, amene mumasanthula maganizo ndi mitima, thetsani chiwawa cha anthu oyipa ndipo wolungama akhale motetezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ithe mphulupulu ya anthu oipa, ndikupemphani, koma wolungamayo mumkhazikitse: Pakuti woyesa mitima ndi imso ndiye Mulungu wolungama.