Psalms 70:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amandinyodola kuti, “Ha, Ha,” achoke ndi manyazi poona kuti alephera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Abwerere, kukhale mphotho ya manyazi ao amene akuti, Hede, hede.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onse amene akunena kwa ine kuti, “Aha, aha,” abwerere chifukwa cha manyazi awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Abwerere, kukhale mphotho ya manyazi ao Amene akuti, Hede, hede.