Psalms 71:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakamwa panga padzalankhula tsiku lonse za ntchito zanu zolungama ndi za chipulumutso chanu, popeza kuti sindidziŵa chiŵerengero chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakamwa panga padzafotokozera chilungamo chanu, ndi chipulumutso chanu tsiku lonse; pakuti sindidziwa mawerengedwe ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakamwa panga padzafotokoza za chilungamo chanu, za chipulumutso chanu tsiku lonse, ngakhale sindikudziwa muyeso wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakamwa panga padzafotokozera cilungamo canu, Ndi cipulumutso canu tsiku lonse; Pakuti sindidziwa mawerengedwe ace.