Psalms 71:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga, ndipo ndikulalikabe ntchito zanu zodabwitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga; ndipo kufikira lero ndilalikira zodabwitsa zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuyambira ubwana wanga, Inu Mulungu mwakhala mukundiphunzitsa, ndipo mpaka lero ine ndikulengeza za ntchito zanu zodabwitsa
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira ubwana wanga; Ndipo kufikira lero ndilalikira zodabwiza zanu.