Psalms 71:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphamvu zanu ndi kulungama kwanu, zimafikira mpaka kumwambamwamba. Pali yani wofanafana nanu, Inu Mulungu, amene mwachita zazikulu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chilungamo chanunso, Mulungu, chifikira kuthambo; Inu amene munachita zachikulu, akunga Inu ndani, Mulungu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu zanu ndi kulungama kwanu zimafika mpaka kumwambamwamba. Ndani wofanana nanu Inu Mulungu, amene mwachita zazikulu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cilungamo canunso, Mulungu, cifikira kuthambo; Inu amene munacita zazikuru, Akunga Inu ndani, Mulungu?