Psalms 71:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mundilanditse ndi kundipulumutsa, pakuti ndinu Mulungu wolungama. Tcherani khutu kuti mundimve, ndipo mundipulumutse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikwatuleni m'chilungamo chanu, ndi kundilanditsa, nditcherereni khutu lanu ndi kundipulumutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mundilanditse ndi kundipulumutsa mwa chilungamo chanu, mutchere khutu lanu ndi kundipulumutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikwatuleni m'cilungamo canu, ndi kundilanditsa: Ndicherereni khutu lanu ndi kundipulumutsa.