Psalms 71:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzanditsitsimutsanso Inu amene mwandiwonetsa mavuto ambiri oŵaŵa, mudzanditulutsanso m'dzenje lozama la pansi pa nthaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu, amene munationetsa nsautso zambiri ndi zoipa, mudzatipatsanso moyo, ndi kutitenganso munsi mwa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale mwandionetsa mavuto ambiri owawa, mudzabwezeretsanso moyo wanga; kuchokera kunsi kwa dziko lapansi, mudzandiukitsanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu, amene munationetsa nsautso zambiri ndi zoipa, Mudzatipatsanso moyo, Ndi kutitenganso munsi mwa dziko.