Psalms 71:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakutamandaninso ndi zeze, Inu Mulungu wanga, chifukwa cha kukhulupirika kwanu. Ndidzaimba nyimbo zoyamika Inu ndi pangwe, Inu Woyera wa Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso ndidzakuyamikani ndi chisakasa, kubukitsa choonadi chanu, Mulungu wanga; ndidzakuimbirani nyimbo ndi zeze, ndinu Woyerayo wa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutamandani ndi zeze chifukwa cha kukhulupirika kwanu Mulungu, ndidzayimba matamando kwa Inu ndi pangwe, Inu Woyera wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso ndidzakuyamikani ndi cisakasa, Kubukitsa coonadi canu, Mulungu wanga; Ndidzakuyimbirani Nyimbo ndi zeze, Ndinu Woyerayo wa Israyeli.