Psalms 71:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lonse ndidzasimba za kulungama kwanu, pakuti amene ankafuna kundichita choipa, aŵachititsa manyazi ndipo aŵanyazitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lilime langa lomwe lidzalankhula za chilungamo chanu tsiku lonse, pakuti ofuna kundichitira choipa achita manyazi, nadodoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lilime langa lidzafotokoza za ntchito zanu zachilungamo tsiku lonse, pakuti iwo amene amafuna kundipweteka achititsidwa manyazi ndi kusokonezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lilime langa lomwe lidzalankhula za cilungamo canu tsiku lonse: Pakuti ofuna kundicitira coipa acita manyazi, nadodoma.