Psalms 71:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Landitseni Inu Mulungu wanga kwa anthu oipa, landitseni ku mphamvu za anthu osalungama ndi ankhalwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndilanditseni, Mulungu wanga, m'dzanja la woipa, m'dzanja la munthu wosalungama ndi wachiwawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Landitseni Inu Mulungu wanga, kuchoka mʼdzanja la oyipa, kuchoka mʼdzanja la oyipa ndi anthu ankhanza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndilanditseni, Mulungu wanga, m'dzanja la woipa, M'dzanja la munthu wosalungama ndi waciwawa.