Psalms 71:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Ambuye, ndinu amene ndimakukhulupirirani, Inu Chauta, ndinu amene ndimakudalirani kuyambira ubwana wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Inu ndinu chiyembekezo changa, Ambuye Yehova; mwandikhalira wokhulupirika kuyambira ubwana wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu mwakhala chiyembekezo changa, Inu Ambuye Wamphamvuzonse, chilimbikitso changa kuyambira ndili mwana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Inu ndinu ciyembekezo canga, Ambuye Yehova; Mwandikhalira wokhulupirika kuyambira ubwana wanga.