Psalms 72:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, patsaniko mfumu nzeru zoweruzira, patsaniko mwana wa mfumu mtima wokonda chilungamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la kwa Solomoni. Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu, ndi mwana wa mfumu chilungamo chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Solomoni. Patsani mwana wa mfumu nzeru zanu zoweruzira mwa chilungamo, Inu Mulungu mupatseni mwana wa mfumu chilungamo chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu, Ndi mwana wa mfumu cilungamo canu.