Psalms 72:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idzamvera chisoni anthu ofooka ndi osoŵa, ndipo idzapulumutsa moyo wa anthu aumphaŵi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzachitira nsoni wosauka ndi waumphawi, nadzapulumutsa moyo wa aumphawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzachitira chifundo anthu ofowoka ndi anthu osowa ndi kupulumutsa osowa ku imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzacitira nsoni wosauka ndi waumphawi, Nadzapulumutsa moyo wa aumphawi,