Psalms 72:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu idzateteza anthu osauka, idzapulumutsa anthu osoŵa, koma idzaononga anthu ozunza anzao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzaweruza ozunzika a mwa anthu, adzapulumutsa ana aumphawi, nadzaphwanya wosautsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzateteza ozunzika pakati pa anthu ndi kupulumutsa ana a anthu osowa; adzaphwanya ozunza anzawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzaweruza ozunzika a mwa anthu, Adzapulumutsa ana aumphawi, Nadzaphwanya wosautsa.