Psalms 72:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idzakhala madalitso ngati mvula yogwa pa minda ngati mvula yowaza pa nthaka!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzanga mvula yakugwa pa udzu wosenga, monga mvula yothirira dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzakhala kugwa kwa mvula pa minda yolimidwa ngati mivumbi yothirira dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzanga mvula yakugwa pa udzu wosenga: Monga mvula yothirira dziko.