Psalms 72:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Idzakhala ikulamulira kuchokera ku nyanja ina mpaka ku nyanja ina, kuchokeranso ku Mtsinje mpaka ku mathero a dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzachita ufumu kuchokera kunyanja kufikira kunyanja, ndi kuchokera ku Mtsinje kufikira malekezero a dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzalamulira kuchokera ku nyanja ina mpaka ku nyanja ina ndiponso kuchokera ku mtsinje mpaka ku malekezero a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzacita ufumu kucokera kunyanja kufikira kunyanja, Ndi kucokera ku Mtsinje kufikira malekezero a dziko lapansi.