Psalms 73:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zoonadi, Mulungu ndi wabwino kwa olungama, kwa anthu oyera mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Asafu. Indedi Mulungu achitira Israele zabwino, iwo a mtima wa mbee.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Asafu. Mulungu ndi wabwino ndithu kwa Israeli, kwa iwo amene ndi oyera mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indedi Mulungu acitira Israyeli zabwino, Iwo a mtima wa mbe.