Psalms 73:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ngakhale anthu a Mulungu amabwera kwa iwo, ndipo amakhuta zonena zao ngati madzi akumwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anthu ake amabwera kudza kuno, ndipo chikho chodzala ndi madzi achigugudiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake anthu awo amapita kwa iwowo ndi kumwa madzi mochuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anthu ace amabwera kudza kuno: Ndipo cikho codzala ndi madzi acigugudiza.