Psalms 73:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndasunga mtima wanga woyera, ndasamba m'manja kuwonetsa kuti ndine wosalakwa, koma zonsezi popanda phindu konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indedi, ndinayeretsa mtima wanga kwachabe, ndipo ndinasamba m'manja mosalakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithudi ine ndawusunga pachabe mtima wanga woyera; pachabe ndasamba mʼmanja mwanga mwa kusalakwa kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indedi, ndinayeretsa mtima wanga kwacabe, Ndipo ndinasamba m'manja mosalakwa;