Psalms 73:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene ndidalingalira zimenezi kuti ndizimvetse bwino, zidandiwonekera ngati nkhani yovuta,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene ndinayesa kudziwitsa ichi, ndinavutika nacho;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinayesa kuti ndimvetse zonsezi, zinandisautsa kwambiri
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene ndinayesa kudziwitsa ici, Ndinabvutika naco;