Psalms 73:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Ambuye, pamene mudzadzuka mudzaŵanyoza kotheratu, monga momwe munthu amanyozera maloto atadzuka m'maŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga anthu atauka, apepula loto; momwemo, Inu Ambuye, pakuuka mudzapeputsa chithunzithunzi chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga loto pamene wina adzuka, kotero pamene Inu muuka, Inu Ambuye, mudzawanyoza ngati maloto chabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga anthu atauka, apepula loto; Momwemo, Inu Ambuye, pakuuka mudzapeputsa cithunzithunzi cao.