Psalms 73:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene paja ndinkavutika ndi maganizo, ndi kumamva cholasa mumtimamu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mtima wanga udawawa, ndipo ndinalaswa m'impso zanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene mtima wanga unasautsidwa ndi kuwawidwa mu mzimu mwanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mtima wanga udawawa, Ndipo ndinalaswa m'imso zanga;