Psalms 73:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndinali wopusa wosamvetsa kanthu, ndinali ngati chilombo kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndinali wam'thengo, wosadziwa kanthu; ndinali ngati nyama pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndinali wopusa ndi wosadziwa; ndinali chirombo chopanda nzeru pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinali wam'thengo, wosadziwa kanthu; Ndinali ngati nyama pamaso panu.