Psalms 73:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga ndili ndi yani kumwamba kupatula Inu? Pansi pano palibe kanthu kena kamene ndimafuna, koma Inu nokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndili ndi yani Kumwamba, koma Inu? Ndipo pa dziko lapansi palibe wina wondikonda koma Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi kumwamba ndili ndi yani kupatula Inu? Ndipo dziko lapansi lilibe chilichonse chimene ndimachilakalaka koposa Inuyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiri ndi yani Kumwamba, koma Inu? Ndipo Pa dziko lapansi palibe wina wondikonda koma Inu.