Psalms 73:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thupi langa ndi mtima wanga zingafooke chotani, Mulungu ndiye mphamvu za mtima wanga ndiyenso wondigaŵira madalitso mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Likatha thupi langa ndi mtima wanga, Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga, ndi cholandira changa chosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Thupi ndi mtima wanga zitha kufowoka, koma Mulungu ndiye mphamvu ya mtima wanga ndi cholandira changa kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Likatha thupi langa ndi mtima wanga: Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga, ndi colandira canga cosatha.