Psalms 73:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onse amene ali kutali ndi Inu adzaonongeka, Inu mumaŵaononga amene ali osakhulupirika kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, taonani, iwo okhala patali ndi Inu adzaonongeka; muononga onse akupembedza kwina, kosiyana ndi Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene ali kutali ndi Inu adzawonongeka; Inu mumawononga onse osakhulupirika pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, taonani, iwo okhala patali ndi Inu adzaonongeka; Muononga onse akupembedza kwina, kosiyana ndi Inu.