Psalms 73:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine kukhala pafupi ndi Mulungu kumandikomera. Ndatsimikiza zoti Ambuye ndiwo kothaŵira kwanga ndipo ndidzalalika ntchito zao zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine, kundikomera kuyandikiza kwa Mulungu. Ndimuyesa Ambuye Yehova pothawirapo ine, kuti ndifotokozere ntchito zanu zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kunena za Ine ndi kwabwino kukhala pafupi ndi Mulungu. Ndatsimikiza kuti Ambuye Yehova ndiwo pothawirapo panga ndipo ndidzalalika ntchito zanu zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine, kundikomera kuyandikiza kwa Mulungu: Ndimuyesa Ambuye Yehova pathawirapo ine, Kuti ndifotokozere nchito zanu zonse,