Psalms 73:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndinkachita nsanje ndi anthu odzikuza, pamene ndidaona anthu oipa akulemera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndinachitira nsanje odzitamandira, pakuona mtendere wa oipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndinkachitira nsanje odzitamandira, pamene ndinaona mtendere wa anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndinacitira nsanje odzitamandira, Pakuona mtendere wa oipa,