Psalms 73:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Saona mavuto monga anthu ena, sazunzika ngati anzao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Savutika monga anthu ena; sasautsika monga anthu ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Saona mavuto monga anthu ena; sazunzika ngati anthu ena onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sabvutika monga anthu ena; Sasautsika monga anthu ena.