Psalms 73:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake amavala kunyada ngati mkanda wam'khosi. Amavala nkhanza ngati malaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake kudzikuza kunga unyolo pakhosi pao; achivala chiwawa ngati malaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake kunyada kuli monga mkanda wa mʼkhosi mwawo; amadziveka chiwawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace kudzikuza kunga unyolo pakhosi pao; Acibvala ciwawa ngati malaya.