Psalms 73:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso ao ndi otupa ndi kunenepa. Mitima yao ndi yodzaza ndi maganizo ofuna kuchita zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunenepa kwao kutuzulitsa maso ao, malingaliro a mitima yao asefukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmitima yawo yokhota mumachokera zolakwa; zoyipa zochokera mʼmaganizo awo sizidziwa malire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunenepa kwao kutuzulitsa maso ao: Malingaliro a mitima yao asefukira.