Psalms 73:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amanyodola ndi kumalankhula zoipa, amadzikuza ndi kumaopseza ena kuti, “Tikupsinjani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Achita zaphwete nalankhula moipa za kusautsa, alankhula modzitama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwowo amanyogodola ndi kumayankhula zoyipa; mwa kudzikuza kwawo amaopseza ena nʼkumati, “Tikuponderezani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Acita zaphwete nalankhula moipa za kusautsa: Alankhula modzitama.