Psalms 73:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakamwa pao pamalankhula monyoza Mulungu kumwamba, ndipo lilime lao ndi losamangika pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakamwa pao anena zam'mwamba, ndipo lilime lao liyendayenda m'dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakamwa pawo pamayankhula monyoza Mulungu kumwamba ndipo lilime lawo limayenda pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakamwa pao anena zam'mwamba, Ndipo lilime lao liyendayenda m'dziko lapansi.