Psalms 74:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, chifukwa chiyani mukutitaya mpaka muyaya? Chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukutukutirira nkhosa za busa lanu ngati moto?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chilangizo cha Asafu. Mulungu, munatitayiranji chitayire? Mkwiyo wanu ufukiranji pa nkhosa za kubusa kwanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakatulo ya Asafu. Nʼchifukwa chiyani mwatitaya ife kwamuyaya, Inu Mulungu? Chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukutukutira pa nkhosa za busa lanu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu, munatitayiranji citayire? Mkwiyo wanu ufukiranji pa nkhosa za kubusa kwanu?