Psalms 74:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mukubisa dzanja lanu lotithandiza? Bwanji dzanja lanu lamanja likungokhala pachifuwa panu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mubwezeranji dzanja lanu, ndilo dzanja lamanja lanu? Mulitulutse kuchifuwa chanu ndipo muwatheretu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani mukubweza dzanja lanu lamanja? Litulutseni kuchoka pachifuwa chanu ndipo muwawononge!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mubwezeranji dzanja lanu, ndilo dzanja lamanja lanu? Muliturutse ku cifuwa canu ndipo muwatheretu.