Psalms 74:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Inu Mulungu, ndinu mfumu yanga kuyambira kalekale. Ndinu amene mumagwira ntchito yopulumutsa pa dziko lonse lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Mulungu ndiye mfumu yanga kuyambira kale, wochita zakupulumutsa pakati pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Mulungu, ndinu Mfumu yanga kuyambira kalekale; Mumabweretsa chipulumutso pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Mulungu ndiye mfumu yanga kuyambira kale, Wocita zakupulumutsa pakati pa dziko lapansi.