Psalms 74:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudagaŵa Nyanja Yofiira ndi mphamvu zanu. Mudaphwanya mitu ya zilombo zam'madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudagawa nyanja ndi mphamvu yanu; mudaswa mitu ya zoopsa za m'madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinu amene munagawa nyanja ndi mphamvu yanu; munathyola mitu ya zirombo za mʼmadzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudagawa nyanja ndi mphamvu yanu; Mudaswa mitu ya zoopsa za m'madzi.